Yesaya 41:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Tionetseni ndipo mutiuze zinthu zimene zidzachitike. Tiuzeni kuti zinthu zoyambirira zinali zotani, kuti tiziganizire mozama mumtima mwathu ndi kudziwa tsogolo lake. Kapena mutiuze zinthu zimene zikubwera.+
22 “Tionetseni ndipo mutiuze zinthu zimene zidzachitike. Tiuzeni kuti zinthu zoyambirira zinali zotani, kuti tiziganizire mozama mumtima mwathu ndi kudziwa tsogolo lake. Kapena mutiuze zinthu zimene zikubwera.+