Deuteronomo 4:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Inu mukudziwa bwino lero, ndipo muzikumbukira m’mitima yanu, kuti Yehova ndiye Mulungu woona, kumwamba ndiponso padziko lapansi.+ Palibenso wina.+ Yoweli 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndili pakati pa Isiraeli,+ ndiponso kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu ndipo palibenso Mulungu wina.+ Anthu anga sadzachita manyazi mpaka kalekale.
39 Inu mukudziwa bwino lero, ndipo muzikumbukira m’mitima yanu, kuti Yehova ndiye Mulungu woona, kumwamba ndiponso padziko lapansi.+ Palibenso wina.+
27 Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndili pakati pa Isiraeli,+ ndiponso kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu ndipo palibenso Mulungu wina.+ Anthu anga sadzachita manyazi mpaka kalekale.