Deuteronomo 28:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 “Chotero, monga mmene Yehova anasangalalira kuti akuchitireni zabwino ndi kukuchulukitsani,+ momwemonso adzasangalala kuti akuwonongeni ndi kukufafanizani.+ Pamenepo mudzatheratu m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.+ Yeremiya 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Inu mwaona masoka onse amene ndagwetsera Yerusalemu+ ndi mizinda yonse ya Yuda. Lero mizinda imeneyi yakhala mabwinja ndipo palibe amene akukhalamo.+
63 “Chotero, monga mmene Yehova anasangalalira kuti akuchitireni zabwino ndi kukuchulukitsani,+ momwemonso adzasangalala kuti akuwonongeni ndi kukufafanizani.+ Pamenepo mudzatheratu m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.+
2 “Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Inu mwaona masoka onse amene ndagwetsera Yerusalemu+ ndi mizinda yonse ya Yuda. Lero mizinda imeneyi yakhala mabwinja ndipo palibe amene akukhalamo.+