Salimo 64:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama adzakondwera mwa Yehova ndipo adzathawira kwa iye,+Ndipo onse owongoka mtima adzatamanda Mulungu.+ 2 Akorinto 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Koma amene akudzitamandira, adzitamande mwa Yehova.”+
10 Wolungama adzakondwera mwa Yehova ndipo adzathawira kwa iye,+Ndipo onse owongoka mtima adzatamanda Mulungu.+