Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:63
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 63 “Chotero, monga mmene Yehova anasangalalira kuti akuchitireni zabwino ndi kukuchulukitsani,+ momwemonso adzasangalala kuti akuwonongeni ndi kukufafanizani.+ Pamenepo mudzatheratu m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.+

  • Yesaya 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndidzamutumiza kuti akalimbane ndi mtundu wopanduka,+ ndipo ndidzamulamula kuti akalimbane ndi anthu amene andikwiyitsa. Ndidzamuuza+ kuti akalande zinthu zambiri, akatenge katundu wambiri, ndiponso akapondeponde anthuwo ngati matope a mumsewu.+

  • Ezekieli 24:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 ‘Uza nyumba ya Isiraeli kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndidetsa malo anga opatulika,+ chinthu chimene mumachinyadira kwambiri,+ chinthu chosiririka kwa inu,+ ndiponso chinthu chimene mumachichitira chifundo. Ana anu aamuna ndi aakazi amene munawasiya m’mbuyo adzaphedwa ndi lupanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena