Salimo 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti woipa amadzitamandira ndi zilakolako zake zadyera,+Ndipo wopanga phindu lachinyengo+ amadzitamanda.נ [Nun]Iye amanyoza Yehova.+ Salimo 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa,+ ndipo amachita zinthu zonyansa.Palibe amene akuchita zabwino.+ Salimo 36:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mawu a pakamwa pake ndi opweteka ndi achinyengo.+Wasiya kugwiritsa ntchito nzeru zomuthandiza kuchita zinthu zabwino.+ Miyambo 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 mtima wokonzera ena ziwembu,+ mapazi othamangira kukachita zoipa,+
3 Pakuti woipa amadzitamandira ndi zilakolako zake zadyera,+Ndipo wopanga phindu lachinyengo+ amadzitamanda.נ [Nun]Iye amanyoza Yehova.+
14 Wopusa amanena mumtima mwake kuti:“Kulibe Yehova.”+Anthu oterewa amachita zoipa,+ ndipo amachita zinthu zonyansa.Palibe amene akuchita zabwino.+
3 Mawu a pakamwa pake ndi opweteka ndi achinyengo.+Wasiya kugwiritsa ntchito nzeru zomuthandiza kuchita zinthu zabwino.+