Yesaya 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu anthu anga amene mwapunthidwa ngati mbewu, ndi iwe mwana wa pamalo anga opunthira mbewu,+ zimene ndamva kwa Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, n’zimene ndakuuzani anthu inu. Yesaya 43:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ine ndanena ndipo ndapulumutsa.+ Pa nthawi imene pakati panu panalibe mulungu wachilendo,+ ine ndinachititsa kuti chipulumutsocho chimveke. Choncho inuyo ndinu mboni zanga,+ ndipo ine ndine Mulungu,” akutero Yehova.+ Mika 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mawu a Yehova akumveka mumzinda.+ Munthu wanzeru zopindulitsa adzaopa dzina lanu.+ Anthu inu, mverani mawu a ndodo ndi a amene anaisankha.+
10 Inu anthu anga amene mwapunthidwa ngati mbewu, ndi iwe mwana wa pamalo anga opunthira mbewu,+ zimene ndamva kwa Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, n’zimene ndakuuzani anthu inu.
12 “Ine ndanena ndipo ndapulumutsa.+ Pa nthawi imene pakati panu panalibe mulungu wachilendo,+ ine ndinachititsa kuti chipulumutsocho chimveke. Choncho inuyo ndinu mboni zanga,+ ndipo ine ndine Mulungu,” akutero Yehova.+
9 Mawu a Yehova akumveka mumzinda.+ Munthu wanzeru zopindulitsa adzaopa dzina lanu.+ Anthu inu, mverani mawu a ndodo ndi a amene anaisankha.+