Salimo 107:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Wanzeru ndani? Iye aona zimenezi,+Ndi kuchita chidwi ndi ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+ Yesaya 41:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndidzachita zimenezi kuti anthu onse pamodzi aone, adziwe, amve, ndiponso azindikire, kuti dzanja la Yehova ndi limene lachita zimenezi, ndiponso kuti Woyera wa Isiraeli ndi amene wachititsa zimenezi.”+
43 Wanzeru ndani? Iye aona zimenezi,+Ndi kuchita chidwi ndi ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+
20 Ndidzachita zimenezi kuti anthu onse pamodzi aone, adziwe, amve, ndiponso azindikire, kuti dzanja la Yehova ndi limene lachita zimenezi, ndiponso kuti Woyera wa Isiraeli ndi amene wachititsa zimenezi.”+