Yesaya 42:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Zinthu zoyamba zachitika,+ koma ndikukuuzani zinthu zatsopano. Zisanayambe kuonekera, ndimakuuzani.”+ 2 Petulo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa ulosi sunayambe wanenedwapo mwa kufuna kwa munthu,+ koma anthu analankhula mawu ochokera kwa Mulungu+ motsogoleredwa ndi mzimu woyera.+
9 “Zinthu zoyamba zachitika,+ koma ndikukuuzani zinthu zatsopano. Zisanayambe kuonekera, ndimakuuzani.”+
21 Chifukwa ulosi sunayambe wanenedwapo mwa kufuna kwa munthu,+ koma anthu analankhula mawu ochokera kwa Mulungu+ motsogoleredwa ndi mzimu woyera.+