Yesaya 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti Yehova wakukhuthulirani mzimu wa tulo tatikulu+ ndipo watseka maso anu, omwe ndi aneneri.+ Waphimba mitu yanu,+ imene ndi anthu amasomphenya.+
10 Pakuti Yehova wakukhuthulirani mzimu wa tulo tatikulu+ ndipo watseka maso anu, omwe ndi aneneri.+ Waphimba mitu yanu,+ imene ndi anthu amasomphenya.+