Salimo 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu munati: “Ndidzakupatsa nzeru ndi kukulangiza njira yoti uyendemo.+Ndidzakupatsa malangizo ndi kukuyang’anira.+ Yesaya 30:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Makutu ako adzamva mawu kumbuyo kwako, akuti: “Njira ndi iyi.+ Yendani mmenemu anthu inu.” Yendani m’njira imeneyi kuti musasochere n’kulowera kudzanja lamanja kapena lamanzere.+ Yesaya 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo sadzakhala ndi njala+ ndipo sadzamva ludzu.+ Sadzamva kutentha kapena kupsa ndi dzuwa.+ Pakuti yemwe amawamvera chisoni adzawatsogolera+ ndipo adzapita nawo ku akasupe amadzi.+
8 Inu munati: “Ndidzakupatsa nzeru ndi kukulangiza njira yoti uyendemo.+Ndidzakupatsa malangizo ndi kukuyang’anira.+
21 Makutu ako adzamva mawu kumbuyo kwako, akuti: “Njira ndi iyi.+ Yendani mmenemu anthu inu.” Yendani m’njira imeneyi kuti musasochere n’kulowera kudzanja lamanja kapena lamanzere.+
10 Iwo sadzakhala ndi njala+ ndipo sadzamva ludzu.+ Sadzamva kutentha kapena kupsa ndi dzuwa.+ Pakuti yemwe amawamvera chisoni adzawatsogolera+ ndipo adzapita nawo ku akasupe amadzi.+