Yeremiya 51:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 “Tamverani! Ku Babulo kukumveka kulira kofuula+ ndipo m’dziko la Akasidi mukumveka phokoso la chiwonongeko chachikulu,+
54 “Tamverani! Ku Babulo kukumveka kulira kofuula+ ndipo m’dziko la Akasidi mukumveka phokoso la chiwonongeko chachikulu,+