2 Mbiri 36:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova Mulungu wa makolo awo anapitiriza kuwatumizira machenjezo kudzera mwa amithenga ake.+ Anawatumiza mobwerezabwereza chifukwa ankamvera chisoni anthu akewo+ ndiponso malo ake okhala.+ Aroma 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Komanso, Yesaya analankhula mofuula zokhudza Isiraeli kuti: “Ngakhale kuti ana a Isiraeli adzakhala ochuluka ngati mchenga wa m’nyanja,+ ndi ochepa okha amene adzapulumuke.+ Aroma 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yesaya analankhula molimba mtima kwambiri kuti: “Anthu amene anandipeza ndi amene sanali kundifunafuna.+ Ndinaonekera kwa anthu amene sanafunse za ine kuti andipeze.”+
15 Yehova Mulungu wa makolo awo anapitiriza kuwatumizira machenjezo kudzera mwa amithenga ake.+ Anawatumiza mobwerezabwereza chifukwa ankamvera chisoni anthu akewo+ ndiponso malo ake okhala.+
27 Komanso, Yesaya analankhula mofuula zokhudza Isiraeli kuti: “Ngakhale kuti ana a Isiraeli adzakhala ochuluka ngati mchenga wa m’nyanja,+ ndi ochepa okha amene adzapulumuke.+
20 Koma Yesaya analankhula molimba mtima kwambiri kuti: “Anthu amene anandipeza ndi amene sanali kundifunafuna.+ Ndinaonekera kwa anthu amene sanafunse za ine kuti andipeze.”+