Mateyu 26:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Kenako anayamba kumulavulira kunkhope+ ndi kum’menya+ nkhonya. Ena anamuwomba mbama,+