Maliko 10:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pakuti ngakhale Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa,+ koma kudzatumikira ndi kudzapereka moyo wake dipo+ kuwombola anthu ambiri.”+ Luka 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kodi wamkulu ndani, amene akudya patebulo kapena amene akutumikira? Si amene akudya patebulo kodi? Koma ine ndili pakati panu monga wotumikira.+
45 Pakuti ngakhale Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa,+ koma kudzatumikira ndi kudzapereka moyo wake dipo+ kuwombola anthu ambiri.”+
27 Kodi wamkulu ndani, amene akudya patebulo kapena amene akutumikira? Si amene akudya patebulo kodi? Koma ine ndili pakati panu monga wotumikira.+