Deuteronomo 28:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anthu amene sunawadziwe adzadya zipatso za m’dziko lako ndi mbewu zako zonse.+ Motero udzakhala wodyeredwa ndi woponderezedwa nthawi zonse.+ 2 Mafumu 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 M’masiku amenewo, Yehova anayamba kulanda dziko la Isiraeli pang’ono ndi pang’ono, ndipo Hazaeli+ anapitiriza kupha anthu m’madera onse a dziko la Isiraeli.
33 Anthu amene sunawadziwe adzadya zipatso za m’dziko lako ndi mbewu zako zonse.+ Motero udzakhala wodyeredwa ndi woponderezedwa nthawi zonse.+
32 M’masiku amenewo, Yehova anayamba kulanda dziko la Isiraeli pang’ono ndi pang’ono, ndipo Hazaeli+ anapitiriza kupha anthu m’madera onse a dziko la Isiraeli.