Yobu 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pansi, mizu yake idzauma.+Pamwamba, nthambi yake idzafota. Hoseya 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Efuraimu adzavulazidwa.+ Muzu wake udzauma,+ ndipo sadzaberekanso chipatso chilichonse.+ Komanso ngati angabereke, ndidzapha chipatso chokondedwa cha mimba yawo.”+ Amosi 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Koma ine ndinawononga Aamori+ chifukwa cha anthu anga. Aamoriwo misinkhu yawo inali yofanana ndi mitengo ya mkungudza ndipo mphamvu zawo zinali zofanana ndi za mitengo ikuluikulu.+ Ndinawononga zipatso zawo m’mwamba ndiponso mizu yawo pansi.+
16 Efuraimu adzavulazidwa.+ Muzu wake udzauma,+ ndipo sadzaberekanso chipatso chilichonse.+ Komanso ngati angabereke, ndidzapha chipatso chokondedwa cha mimba yawo.”+
9 “‘Koma ine ndinawononga Aamori+ chifukwa cha anthu anga. Aamoriwo misinkhu yawo inali yofanana ndi mitengo ya mkungudza ndipo mphamvu zawo zinali zofanana ndi za mitengo ikuluikulu.+ Ndinawononga zipatso zawo m’mwamba ndiponso mizu yawo pansi.+