Mateyu 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kapena munthu angalowe bwanji m’nyumba ya munthu wamphamvu ndi kulanda katundu wake, ngati sangamange munthu wamphamvuyo choyamba? Atam’manga, m’pamene angathe kutenga katundu m’nyumbamo.+ Luka 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu wamphamvu,+ wokhala ndi zida zokwanira, akamalondera nyumba yake, chuma chake chimatetezeka.
29 Kapena munthu angalowe bwanji m’nyumba ya munthu wamphamvu ndi kulanda katundu wake, ngati sangamange munthu wamphamvuyo choyamba? Atam’manga, m’pamene angathe kutenga katundu m’nyumbamo.+
21 Munthu wamphamvu,+ wokhala ndi zida zokwanira, akamalondera nyumba yake, chuma chake chimatetezeka.