Salimo 40:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nsembe ndiponso zopereka, simunasangalale nazo.+Inu munatsegula makutu anga.+Simunapemphe nsembe yopsereza ndi nsembe yamachimo.+ Salimo 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimakondwera ndi kuchita chifuniro chanu, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+
6 Nsembe ndiponso zopereka, simunasangalale nazo.+Inu munatsegula makutu anga.+Simunapemphe nsembe yopsereza ndi nsembe yamachimo.+
8 Ndimakondwera ndi kuchita chifuniro chanu, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+