Salimo 105:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nyadirani dzina lake loyera.+Mtima wa anthu ofunafuna Yehova usangalale.+ Aroma 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti “aliyense amene adzaitana pa dzina la Yehova* adzapulumuka.”+