Genesis 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Sara anakhala ndi pakati+ n’kuberekera Abulahamu mwana, Abulahamuyo atakalamba. Izi zinachitika pa nthawi yoikidwiratu imene Mulungu analonjeza Abulahamu.+
2 Choncho Sara anakhala ndi pakati+ n’kuberekera Abulahamu mwana, Abulahamuyo atakalamba. Izi zinachitika pa nthawi yoikidwiratu imene Mulungu analonjeza Abulahamu.+