Yeremiya 31:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yehova ndiye Wopereka dzuwa kuti liziwala masana,+ woikira mwezi malamulo,+ wopereka nyenyezi+ kuti ziziwala usiku,+ amene amavundula nyanja kuti mafunde ake achite phokoso.+ Wochita zimenezi dzina lake ndi Yehova wa makamu.+ Iye wanena kuti: Yona 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yehova anabweretsa chimphepo champhamvu panyanjapo,+ ndipo panachita mkuntho wamphamvu.+ Chotero chombocho chinatsala pang’ono kusweka.
35 Yehova ndiye Wopereka dzuwa kuti liziwala masana,+ woikira mwezi malamulo,+ wopereka nyenyezi+ kuti ziziwala usiku,+ amene amavundula nyanja kuti mafunde ake achite phokoso.+ Wochita zimenezi dzina lake ndi Yehova wa makamu.+ Iye wanena kuti:
4 Ndiyeno Yehova anabweretsa chimphepo champhamvu panyanjapo,+ ndipo panachita mkuntho wamphamvu.+ Chotero chombocho chinatsala pang’ono kusweka.