Deuteronomo 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yehova adzakulanga ndi misala,+ khungu+ ndipo adzakuchititsa kudabwa kwambiri.+ Salimo 60:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu anu mwawaonetsa zovuta.+Mwatimwetsa vinyo ndipo tikuyenda dzandidzandi.+