Chivumbulutso 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo ndinaona kuti mkaziyo anali ataledzera ndi magazi+ a oyera, ndiponso magazi a mboni za Yesu.+ Nditamuona mkaziyo, ndinadabwa kwambiri.+
6 Ndipo ndinaona kuti mkaziyo anali ataledzera ndi magazi+ a oyera, ndiponso magazi a mboni za Yesu.+ Nditamuona mkaziyo, ndinadabwa kwambiri.+