Salimo 44:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwagulitsa anthu anu pa mtengo wotsika kwambiri,+Ndipo simunapeze phindu ndi mtengo wawo.