44 Ndikadzachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa,+ inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.+ Inu a nyumba ya Isiraeli, ine sindidzachitapo kanthu mogwirizana ndi njira zanu zoipa kapena zochita zanu zosayenera,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”