Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Zekariya 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Posonyeza kuti ndakomera mtima nyumba ya Davide ndi anthu okhala mu Yerusalemu, ndidzawapatsa mzimu wanga+ umene udzawalimbikitse kundipempha mochonderera.+ Ndithu iwo adzayang’ana kwa munthu amene anamulasa,+ ndipo adzamulirira ngati mmene amachitira polirira mwana yekhayo wamwamuna. Adzamulira mowawidwa mtima ngati mmene amachitira polira maliro a mwana wamwamuna woyamba kubadwa.+

  • Mateyu 27:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Koma enawo anati: “Mulekeni! Tione ngati Eliya angabwere kudzam’pulumutsa.”+ [[Munthu wina anatenga mkondo ndi kumubaya* m’mbalimu cham’mimba ndipo panatuluka magazi ndi madzi.]]*+

  • Yohane 19:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Koma mmodzi wa asilikaliwo anamulasa ndi mkondo m’mbalimu cham’mimba,+ ndipo nthawi yomweyo panatuluka magazi ndi madzi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena