Mateyu 27:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano anthu odutsa anayamba kunena mawu onyoza+ Yesu. Anali kupukusa+ mitu yawo Mateyu 27:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Chimodzimodzinso ansembe aakulu limodzi ndi alembi komanso akulu. Nawonso anayamba kum’chita chipongwe ndi kunena kuti:+ Yohane 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano Pilato anatenga Yesu ndi kumukwapula.+ 1 Petulo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene anali kunenedwa zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene anali kuvutika,+ sanawopseze, koma anali kudzipereka kwa iye+ amene amaweruza molungama.
41 Chimodzimodzinso ansembe aakulu limodzi ndi alembi komanso akulu. Nawonso anayamba kum’chita chipongwe ndi kunena kuti:+
23 Pamene anali kunenedwa zachipongwe,+ sanabwezere zachipongwe.+ Pamene anali kuvutika,+ sanawopseze, koma anali kudzipereka kwa iye+ amene amaweruza molungama.