Machitidwe 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+ Machitidwe 7:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Ndi mneneri uti amene makolo anuwo sanamuzunze?+ Inde, iwo anapha+ amene analengezeratu za kubwera kwa Wolungamayo,+ amene inuyo munamupereka ndi kumupha,+
15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+
52 Ndi mneneri uti amene makolo anuwo sanamuzunze?+ Inde, iwo anapha+ amene analengezeratu za kubwera kwa Wolungamayo,+ amene inuyo munamupereka ndi kumupha,+