Genesis 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzaika+ chidani+ pakati pa iwe+ ndi mkaziyo,+ ndi pakati pa mbewu yako+ ndi mbewu yake.+ Mbewu ya mkaziyo+ idzaphwanya mutu wako,+ ndipo iwe+ udzaivulaza chidendene.”+ Luka 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Komanso, Simiyoni anadalitsa makolowo, ndipo anauza Mariya, mayi a mwanayo kuti: “Tamverani! Uyu waikidwa kuti ambiri agwe,+ ndiponso kuti ambiri adzukenso mu Isiraeli,+ ndi kuti akhale chizindikiro chimene anthu adzachitsutse+
15 Ndidzaika+ chidani+ pakati pa iwe+ ndi mkaziyo,+ ndi pakati pa mbewu yako+ ndi mbewu yake.+ Mbewu ya mkaziyo+ idzaphwanya mutu wako,+ ndipo iwe+ udzaivulaza chidendene.”+
34 Komanso, Simiyoni anadalitsa makolowo, ndipo anauza Mariya, mayi a mwanayo kuti: “Tamverani! Uyu waikidwa kuti ambiri agwe,+ ndiponso kuti ambiri adzukenso mu Isiraeli,+ ndi kuti akhale chizindikiro chimene anthu adzachitsutse+