Luka 22:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Koma atazunzika koopsa mumtima mwake, anapitiriza kupemphera ndi mtima wonse+ ndipo thukuta lake linaoneka ngati madontho amagazi amene akugwera pansi.+
44 Koma atazunzika koopsa mumtima mwake, anapitiriza kupemphera ndi mtima wonse+ ndipo thukuta lake linaoneka ngati madontho amagazi amene akugwera pansi.+