Yeremiya 31:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “‘Ngati malamulo amenewa angachotsedwe pamaso panga,+ ndiye kuti anthu amene ndi mbewu ya Isiraeli sadzakhala mtundu wokhala pamaso panga nthawi zonse,’+ watero Yehova.” Ezekieli 39:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Sindidzawabisiranso nkhope yanga+ chifukwa panyumba ya Isiraeli, ndidzatsanulirapo mzimu wanga,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
36 “‘Ngati malamulo amenewa angachotsedwe pamaso panga,+ ndiye kuti anthu amene ndi mbewu ya Isiraeli sadzakhala mtundu wokhala pamaso panga nthawi zonse,’+ watero Yehova.”
29 Sindidzawabisiranso nkhope yanga+ chifukwa panyumba ya Isiraeli, ndidzatsanulirapo mzimu wanga,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”