Maliro 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye akulira kwambiri usiku,+ ndipo misozi ikutsika pamasaya ake.+Pakati pa onse amene anali kumukonda, palibe amene akumutonthoza.+Anthu onse amene anali anzake amuchitira zachinyengo+ ndipo akhala adani ake.+ Maliro 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ziyoni watambasula manja ake.+ Iye alibe womutonthoza.+Yehova walamula onse ozungulira Yakobo kuti akhale adani ake.+Yerusalemu wakhala chinthu chonyansa pakati pawo.+
2 Iye akulira kwambiri usiku,+ ndipo misozi ikutsika pamasaya ake.+Pakati pa onse amene anali kumukonda, palibe amene akumutonthoza.+Anthu onse amene anali anzake amuchitira zachinyengo+ ndipo akhala adani ake.+
17 Ziyoni watambasula manja ake.+ Iye alibe womutonthoza.+Yehova walamula onse ozungulira Yakobo kuti akhale adani ake.+Yerusalemu wakhala chinthu chonyansa pakati pawo.+