Chivumbulutso 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mzindawo unali ndi mpanda waukulu ndi wautali,+ ndipo unali ndi zipata 12. Pazipatazo panali angelo 12, ndipo panalembedwa mayina a mafuko 12 a ana a Isiraeli.+
12 Mzindawo unali ndi mpanda waukulu ndi wautali,+ ndipo unali ndi zipata 12. Pazipatazo panali angelo 12, ndipo panalembedwa mayina a mafuko 12 a ana a Isiraeli.+