Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 49:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Ndimvereni zilumba inu,+ ndipo mvetserani, inu mitundu ya anthu akutali.+ Yehova anandiitana+ ndili m’mimba.+ Ndili mkati mwa mayi anga, anatchula dzina langa.+

  • Yesaya 51:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Inu anthu anga, tandimverani. Iwe mtundu wanga,+ tatchera khutu kwa ine. Pakuti kwa ine kudzachokera lamulo+ ndipo ndidzachititsa chigamulo changa kukhazikika monga kuwala kwa mitundu ya anthu.+

  • Danieli 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako anamupatsa ulamuliro,+ ulemerero,+ ndi ufumu+ kuti anthu a mitundu yosiyanasiyana, olankhula zinenero zosiyanasiyana azimutumikira.+ Ulamuliro wake udzakhalapo mpaka kalekale ndipo sudzatha. Ufumu wake sudzawonongedwa.+

  • Mika 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anthu ochokera m’mitundu yosiyanasiyana adzabwera n’kunena kuti: “Bwerani+ anthu inu. Tiyeni tipite kukakwera phiri la Yehova. Tipite kunyumba ya Mulungu wa Yakobo.+ Iye akatiphunzitsa njira zake,+ ndipo ife tidzayenda m’njira zakezo.”+ Pakuti mu Ziyoni mudzatuluka malamulo ndipo mawu a Yehova adzatuluka mu Yerusalemu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena