Levitiko 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Mukapitiriza kutsatira malangizo anga ndi kusunga malamulo anga,+ Miyambo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gwira malangizo,+ usawataye.+ Uwasunge bwino chifukwa iwo ndiwo moyo wako.+