Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 19:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pakuti ena sakwatira chifukwa chakuti anabadwa choncho kuchokera m’mimba mwa mayi awo,+ ndipo ena chifukwa chakuti anafulidwa ndi anthu. Koma pali ena amene safuna kukwatira chifukwa cha ufumu wakumwamba. Amene angathe kuchita zimenezi achite.”+

  • 1 Akorinto 7:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Nayenso amene walekana ndi moyo wokhala yekha* n’kulowa m’banja wachita bwino,+ koma amene sanalowe m’banja wachita bwino koposa.+

  • 2 Akorinto 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndiye chifukwa chake kuyambira tsopano sitiona munthu mwakuthupi.+ Ngakhale kuti Khristu tinamuona mwakuthupi,+ tsopano sitikumuonanso motero.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena