Salimo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Adzachititsa ofatsa kutsatira zigamulo zake,+Ndipo adzaphunzitsa ofatsa kuyenda m’njira yake.+ Salimo 73:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mudzanditsogolera ndi malangizo anu,+Ndipo pambuyo pake mudzanditenga ndi kundipatsa ulemerero.+