Nehemiya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Sanibalati,+ Tobia,+ Gesemu+ Mluya+ ndi adani athu onse atangouzidwa kuti ndamanganso mpanda,+ ndipo palibe mpata umene watsala (ngakhale kuti kufikira pa nthawiyo ndinali ndisanaike zitseko+ m’zipata zake),+ Amosi 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Pa tsiku limenelo, ndidzautsa+ nyumba+ ya Davide imene inagwa,+ ndi kukonza mmene khoma* lake linawonongeka. Ndidzautsa mabwinja ake ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati masiku akale.+
6 Ndiyeno Sanibalati,+ Tobia,+ Gesemu+ Mluya+ ndi adani athu onse atangouzidwa kuti ndamanganso mpanda,+ ndipo palibe mpata umene watsala (ngakhale kuti kufikira pa nthawiyo ndinali ndisanaike zitseko+ m’zipata zake),+
11 “‘Pa tsiku limenelo, ndidzautsa+ nyumba+ ya Davide imene inagwa,+ ndi kukonza mmene khoma* lake linawonongeka. Ndidzautsa mabwinja ake ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati masiku akale.+