2 Mafumu 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamapeto pake, Hoshiya+ mwana wa Ela anakonzera chiwembu+ Peka mwana wa Remaliya n’kumupha.+ Kenako iye anayamba kulamulira m’malo mwake m’chaka cha 20 cha Yotamu+ mwana wa Uziya. Yesaya 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Popeza anthu awa akana+ madzi a ku Silowa+ amene amayenda pang’onopang’ono, ndipo atengeka+ ndi Rezini ndiponso mwana wa Remaliya,+
30 Pamapeto pake, Hoshiya+ mwana wa Ela anakonzera chiwembu+ Peka mwana wa Remaliya n’kumupha.+ Kenako iye anayamba kulamulira m’malo mwake m’chaka cha 20 cha Yotamu+ mwana wa Uziya.
6 “Popeza anthu awa akana+ madzi a ku Silowa+ amene amayenda pang’onopang’ono, ndipo atengeka+ ndi Rezini ndiponso mwana wa Remaliya,+