Salimo 147:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye amachiritsa+ anthu osweka mtima,+Ndipo amamanga zilonda zawo zopweteka.+ 2 Akorinto 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komabe Mulungu, amene amalimbikitsa+ osautsika mtima, anatilimbikitsa ndi kukhalapo* kwa Tito.