Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 102:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kuti amve kuusa moyo kwa akaidi,+

      Ndi kumasula anthu opita kukaphedwa.+

  • Yeremiya 34:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Yehova anauza Yeremiya mawu pamene Mfumu Zedekiya inachita pangano ndi anthu onse a mu Yerusalemu kuti alengeze ufulu,+

  • Aroma 8:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 chakuti chilengedwecho+ chidzamasulidwa+ ku ukapolo wa kuvunda n’kukhala ndi ufulu waulemerero wa ana a Mulungu.

  • Agalatiya 4:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Tsopano, Hagara ameneyu akutanthauza Sinai,+ phiri la ku Arabiya, ndipo masiku ano akufanana ndi Yerusalemu, pakuti ali mu ukapolo+ pamodzi ndi ana ake.

  • Aheberi 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Anachitanso zimenezi kuti amasule+ onse amene poopa imfa,+ anali mu ukapolo moyo wawo wonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena