Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 24:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 “Ndani kwenikweni amene ali kapolo wokhulupirika ndi wanzeru+ amene mbuye wake anamuika kuti aziyang’anira antchito ake apakhomo, ndi kuwapatsa chakudya pa nthawi yoyenera?+

  • Machitidwe 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamene anali kutumikira+ Yehova ndi kusala kudya, mzimu woyera unati: “Mwa anthu onse, mundipatulire Baranaba ndi Saulo+ kuti agwire ntchito imene ndinawaitanira.”

  • Aheberi 10:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Komanso, wansembe aliyense amaima pamalo ake+ kuti achite ntchito yotumikira ena ndi kupereka nsembe zimodzimodzizo mobwerezabwereza,+ popeza zimenezi sizingachotseretu machimo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena