Salimo 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mudzandidziwitsa njira ya moyo.+Chifukwa cha nkhope yanu, munthu adzakondwera mokwanira.+Kudzanja lanu lamanja kuli chimwemwe mpaka muyaya.+ Yesaya 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu owomboledwa ndi Yehova adzabwerera+ n’kukafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Iwo azidzasangalala mpaka kalekale.+ Adzakhala okondwa ndi osangalala ndipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+
11 Mudzandidziwitsa njira ya moyo.+Chifukwa cha nkhope yanu, munthu adzakondwera mokwanira.+Kudzanja lanu lamanja kuli chimwemwe mpaka muyaya.+
10 Anthu owomboledwa ndi Yehova adzabwerera+ n’kukafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Iwo azidzasangalala mpaka kalekale.+ Adzakhala okondwa ndi osangalala ndipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+