1 Samueli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Hana anayamba kupemphera+ kuti:“Mtima wanga ukukondwera mwa Yehova,+Nyanga* yanga yakwezekadi kudzera mwa Yehova.+Ndikutsutsana ndi adani anga molimba mtima,Pakuti ndikukondwera ndi chipulumutso chochokera kwa inu.+ Aroma 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo si zokhazo, koma tikukondweranso mwa Mulungu kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, amene tayanjanitsidwa ndi Mulungu kudzera mwa iye.+
2 Ndiyeno Hana anayamba kupemphera+ kuti:“Mtima wanga ukukondwera mwa Yehova,+Nyanga* yanga yakwezekadi kudzera mwa Yehova.+Ndikutsutsana ndi adani anga molimba mtima,Pakuti ndikukondwera ndi chipulumutso chochokera kwa inu.+
11 Ndipo si zokhazo, koma tikukondweranso mwa Mulungu kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, amene tayanjanitsidwa ndi Mulungu kudzera mwa iye.+