Yesaya 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense adzagwira m’bale wake m’nyumba mwa bambo ake n’kumuuza kuti: “Iwe uli ndi nsalu. Choncho ukhale wolamulira+ wathu ndipo uzilamulira mulu wa bwinjawu.”
6 Aliyense adzagwira m’bale wake m’nyumba mwa bambo ake n’kumuuza kuti: “Iwe uli ndi nsalu. Choncho ukhale wolamulira+ wathu ndipo uzilamulira mulu wa bwinjawu.”