Yesaya 59:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye ataona kuti panalibe munthu aliyense woti n’kuthandizapo, anadabwa kwambiri poona kuti palibe amene akulowererapo.+ Chotero anapulumutsa anthu ndi dzanja lake, ndipo chilungamo chake n’chimene chinamulimbikitsa kuchita zimenezo.+
16 Iye ataona kuti panalibe munthu aliyense woti n’kuthandizapo, anadabwa kwambiri poona kuti palibe amene akulowererapo.+ Chotero anapulumutsa anthu ndi dzanja lake, ndipo chilungamo chake n’chimene chinamulimbikitsa kuchita zimenezo.+