Ekisodo 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ndimasonyeza kukoma mtima kosatha ku mibadwo masauzande chifukwa cha anthu amene amandikonda ndi kusunga malamulo anga.+ Salimo 63:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha n’kwabwino kuposa moyo,+Milomo yanga idzakuyamikirani.+ Salimo 107:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu ayamike Yehova chifukwa cha kukoma mtima kwake kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ntchito zake zodabwitsa zimene wachitira ana a anthu.+ Salimo 136:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 136 Yamikani Yehova anthu inu, pakuti iye ndi wabwino:+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
6 Koma ndimasonyeza kukoma mtima kosatha ku mibadwo masauzande chifukwa cha anthu amene amandikonda ndi kusunga malamulo anga.+
8 Anthu ayamike Yehova chifukwa cha kukoma mtima kwake kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ntchito zake zodabwitsa zimene wachitira ana a anthu.+
136 Yamikani Yehova anthu inu, pakuti iye ndi wabwino:+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+