Numeri 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine nditsikira kumeneko+ kudzalankhula nawe.+ Ndidzatengako gawo lina la mzimu+ umene uli pa iwe n’kuuika pa iwo. Pamenepo iwo adzatha kukuthandiza kusenza udindo woyang’anira anthuwo, kuti usausenze wekhawekha.+ Hagai 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ‘Kumbukirani pangano limene ndinapangana nanu pamene munali kutuluka m’dziko la Iguputo.+ Pa nthawi imeneyo ndinakutumizirani mzimu+ wanga kuti ukutsogolereni. Choncho musachite mantha.’”+ Zekariya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu.
17 Ine nditsikira kumeneko+ kudzalankhula nawe.+ Ndidzatengako gawo lina la mzimu+ umene uli pa iwe n’kuuika pa iwo. Pamenepo iwo adzatha kukuthandiza kusenza udindo woyang’anira anthuwo, kuti usausenze wekhawekha.+
5 ‘Kumbukirani pangano limene ndinapangana nanu pamene munali kutuluka m’dziko la Iguputo.+ Pa nthawi imeneyo ndinakutumizirani mzimu+ wanga kuti ukutsogolereni. Choncho musachite mantha.’”+
6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu.