Ekisodo 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa tsiku lachitatu akhale okonzeka, chifukwa pa tsiku lachitatulo Yehova adzatsikira paphiri la Sinai pamaso pa anthu onse.+ Mika 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamverani! Yehova akuchoka pamalo ake,+ ndipo atsika ndi kupondaponda m’malo okwezeka a padziko lapansi.+
11 Pa tsiku lachitatu akhale okonzeka, chifukwa pa tsiku lachitatulo Yehova adzatsikira paphiri la Sinai pamaso pa anthu onse.+
3 Tamverani! Yehova akuchoka pamalo ake,+ ndipo atsika ndi kupondaponda m’malo okwezeka a padziko lapansi.+